BENGO : Hello abusa, muli pa Airtel Money ngat?
ABUSA : Kumwamba kulemekezeke masiku onse, eya atsogoleri ndili pa airtel money angakhaleso pa Mpamba.
BENGO : Apa muli bize ngati?
ABUSA : Ai atsogoleri, Apa ndangomaliza kumene kupempherera nkhosa zanga, banja lanu komanso utumiki wa mpingo onse.
BENGO : Ok, ndimafuna mundithandize kusintha pin code, paja amatani?
ABUSA : Pamsana panu atsogoleri
BENGO : Inunso pamsana panu abusa
Werengani